13 Ndipo Yesu anati kwa kenturiyoyo, Pita, kukhale kwa iwe monga unakhulupirira. Ndipo anaciritsidwa mnyamatayo nthawi yomweyo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 8
Onani Mateyu 8:13 nkhani