Mateyu 8:14 BL92

14 Ndipo pofika Yesu ku nyumba ya Petro, anaona mpongozi wace ali gone, alikudwala malungo.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 8

Onani Mateyu 8:14 nkhani