16 Ndipo pakudza madzulo, anabwera nao kwa Iye anthu ambiri ogwidwa ndi mizimu yoipa; ndipo Iye anaturutsa mizimuyo ndi mau, naciritsa akudwala onse;
Werengani mutu wathunthu Mateyu 8
Onani Mateyu 8:16 nkhani