10 Ndipo panali pamene Iye analinkukhala pacakudya m'nyumba, onani, amisonkho ndi ocimwa ambiri anadza nakhala pansi pamodzi ndi Yesu ndi ophunzira ace.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 9
Onani Mateyu 9:10 nkhani