30 Ndipo maso ao anaphenyuka. Ndipo Yesu anawauzitsa Iwo, nanena, Yang'anirani, asadziwe munthu ali yense.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 9
Onani Mateyu 9:30 nkhani