2 Mafumu 1:10 BL92

10 Nayankha Eliya, nanena ndi mtsogoleriyo, Ndikakhala ine munthu wa Mulungu, utsike mota wakumwamba, nunyeketse iwe ndi makumi asanu ako. Pamenepo unatsika mota kumwamba, nunyeketsa iye ndi makumi asanu ace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 1

Onani 2 Mafumu 1:10 nkhani