2 Mafumu 1:11 BL92

11 Ndipo anabwereza kutuma kwa iye mtsogoleri wina ndi makumi asanu ace. Ndipo iye anayankha nanena naye, Munthu wa Mulungu iwe, itero mfumu, Tsika msanga.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 1

Onani 2 Mafumu 1:11 nkhani