2 Mafumu 1:12 BL92

12 Nayankha Eliya, nanena nao, Ndikakhala ine munthu wa Mulungu, utsike mota wakumwamba, nunyeketse iwe ndi makumi asanu ako. Pamenepo mota wa Mulungu unatsika kumwamba nunyeketsa iye ndi makumi asanu ace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 1

Onani 2 Mafumu 1:12 nkhani