2 Mafumu 10:13 BL92

13 Yehu anakomana nao abale a Ahaziya mfumu ya Yuda, nati, Ndinu ayani? Nati iwo, Ife ndife abale a Ahaziya, tirikutsika kulankhulira ana a mfumu, ndi ana a nyumba yaikuru.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:13 nkhani