2 Mafumu 10:7 BL92

7 Ndipo kunali, powafika kalatayo, anatenga ana a mfumu, nawapha amuna makumi asanu ndi awiri, naika mitu yao m'mitanga, naitumiza kwa iye ku Yezreeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:7 nkhani