2 Mafumu 10:8 BL92

8 Nudza mthenga, numfotokozera, kuti, Abwera nayo mitu va ana a mfumu. Nati iye, Mulunjike miulu iwiri polowera pa cipata kufikira m'mawa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:8 nkhani