9 Ndipo kunali m'ma wa, iye anaturuka, naima, nati kwa anthu onse, Muli olungama inu, taonani, ndinapandukira mbuye wanga ndi kumupha; koma awa onse anawakantha ndani?
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10
Onani 2 Mafumu 10:9 nkhani