2 Mafumu 11:1 BL92

1 Pamene Ataliya mace wa Ahaziya anaona kuti mwana wace wafa, ananyamuka, naononga mbeu yonse yacifumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 11

Onani 2 Mafumu 11:1 nkhani