2 Mafumu 11:11 BL92

11 Ndipo otumikira anakhala ciriri yense ndi zida zace m'manja mwace, kuyambira mbali ya kulamanja kufikira mbali ya kulamanzere ya nyumbayo, ku guwa la nsembe, ndi kunyumba, kuzinga mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 11

Onani 2 Mafumu 11:11 nkhani