12 Atatero, anaturutsa mwana wa mfumu, namuika korona, nampatsa buku la umboni, namlonga ufumu, namdzoza, naomba m'manja, nati, Mfomu ikhale ndi movo.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 11
Onani 2 Mafumu 11:12 nkhani