2 Mafumu 12:1 BL92

1 Caka cacisanu ndi ciwiri ca Yehu, Yoasi analowa ufumu wace; nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la mai wace ndiye Zibiya wa ku Beereseba.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 12

Onani 2 Mafumu 12:1 nkhani