2 Ndipo Yoasi anacita zoongoka pamaso pa Yehova masiku ace onse, m'mene anamlangizira wansembe Yehoyada.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 12
Onani 2 Mafumu 12:2 nkhani