2 Mafumu 13:12 BL92

12 Macitidwe ena tsono a Yoasi, ndi zonse anazicita, ndi mphamvu yace yocita nkhondo nayo pa Amaziya mfumu ya Yuda, sizilembedwa kodi m'buku la macitidwe a mafumu a Israyeli?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 13

Onani 2 Mafumu 13:12 nkhani