2 Mafumu 13:13 BL92

13 Ndipo Yoasi anagona ndi makolo ace, ndi Yerobiamu anakhala pa mpando wacifumu wace; namuika Yoasi m'Samariya pamodzi ndi mafumu a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 13

Onani 2 Mafumu 13:13 nkhani