2 Mafumu 13:3 BL92

3 Ndipo mkwiyo wa Yehova unayaka pa Israyeli, nawapereka m'dzanja la Hazaeli mfumu ya Aramu, ndi m'dzanja la Benihadadi mwana wa Hazaeli, masiku onsewoo

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 13

Onani 2 Mafumu 13:3 nkhani