2 Mafumu 13:4 BL92

4 Koma Yoahazi anapembedza Yehova, Yehova namvera; pakuti anapenya kupsinjika kwace kwa Israyeli m'mene mfumu ya Aramu inawapsinja.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 13

Onani 2 Mafumu 13:4 nkhani