2 Mafumu 13:5 BL92

5 Ndipo Yehova anapatsa Israyeli mpulumutsi, naturuka iwo pansi pa dzanja la Aaramu; nakhala ana a Israyeli m'mahema mwao monga kale.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 13

Onani 2 Mafumu 13:5 nkhani