15 Macitidwe ena tsono a Yoasi adazicita, ndi mphamvu yace, ndi umo analimbana naye Amaziya mfumu ya Yuda, sizilembedwa kodi m'buku la macitidwe a mafumu a Israyeli?
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 14
Onani 2 Mafumu 14:15 nkhani