2 Mafumu 14:19 BL92

19 Ndipo anamcitira ciwembu m'Yerusalemu, nathawira iye ku Lakisi; koma anatumiza akumtsata ku Lakisi, namupha komweko.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 14

Onani 2 Mafumu 14:19 nkhani