27 Ndipo Yehova sadanena kuti adzafafaniza dzina la Israyeli pansi pa thambo; koma anawapulumutsa ndi dzanja la Yerobiamu mwana wa Yoasi.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 14
Onani 2 Mafumu 14:27 nkhani