2 Mafumu 14:29 BL92

29 Ndipo Yerobiamu anagona ndi makolo ace, ndiwo mafumu a Israyeli; nakhala mfumu m'malo mwace Zekariya mwana wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 14

Onani 2 Mafumu 14:29 nkhani