1 Caka ca makumi awiri mphambu zisanu ndi ziwiri ca Yerobiamu mfumu ya Israyeli, Azariya mwana wa Amaziya mfumu ya Yuda analowa ufumu wace.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:1 nkhani