2 Anali wa zaka khumi ndi zisanu ndi cimodzi polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka makumi asanu mphambu ziwiri m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Yekoliya wa ku Yerusalemu.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:2 nkhani