2 Mafumu 14:8 BL92

8 Pamenepo Amaziya anatuma mithenga kwa Yoasi mwana wa Yoahazi mwana wa Yehu mfumu ya Israyeli, ndi kuti, Idzani tionane maso.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 14

Onani 2 Mafumu 14:8 nkhani