12 Awa ndi mau a Yehova anawanena ndi Yehu, ndi kuti, Ana ako kufikira mbadwo wacinai adzakhala pa mpando wacifumu wa Israyeli. Ndipo kunatero momwemo.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:12 nkhani