13 Salumu mwana wa Yabesi analowa ufumu wace caka ca makumi atatu mphambu zisanu ndi zinai ca Uziya mfumu ya Yuda, nakhala mfumu mwezi umodzi m'Samariya.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:13 nkhani