14 Koma anakwera Menahemu mwana wa Gadi kucokera ku Tiriza, nafika ku Samariya, nakantha Salumu mwana wa Yabesi m'Samariya, namupha; nakhala mfumu m'malo mwace.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:14 nkhani