2 Mafumu 15:15 BL92

15 Macitidwe ena tsono a Salumu ndi ciwembu cace anacicita, taonani, zalembedwa m'buku la macitidwe a mafumu a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15

Onani 2 Mafumu 15:15 nkhani