16 Pamenepo Menahemu anakantha Tifisa, ndi onse anali m'mwemo, ndi malire ace kuyambira ku Tiriza; popeza sanamtsegulira pacipata; anaukantha, natumbula akazi onse a pakati okhala m'mwemo.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:16 nkhani