18 Nacita coipa pamaso pa Yehova masiku ace onse, osaleka zolakwa za Yerobiamu mwana wa Nebati, zimene analakwitsa nazo Israyeli.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:18 nkhani