19 Pamenepo Puli mfumu ya Asuri anadza kudzamenyana ndi dziko, koma Menahemu anampatsa Puli matalente a siliva cikwi cimodzi; kuti dzanja lace likhale naye kukhazikitsa ufumu m'dzanja lace.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:19 nkhani