20 Ndipo Menahemu anasonkhetsa Israyeli ndaramazi, nasonkhetsa acuma, yense masekeli makumi asanu a siliva: kuti azipereke kwa mfumu ya Asuri. Nabwerera mfumu ya Asuri osakhala m'dzikomo.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:20 nkhani