23 Caka ca makumi asanu a Azariya mfumu ya Yuda, Pekahiya mwana wa Menahemu analowa ufumu wace wa Israyeli m'Samariya, nakhala mfumu zaka ziwiri.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:23 nkhani