24 Nacita coipa pamaso pa Yehova, sanaleka zolakwa za Yerobiamu mwana wa Nebati, zimene analakwitsa nazo Israyeli.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:24 nkhani