38 Ndipo anagona Yotamu ndi makolo ace, namuika pamodzi ndi makolo ace m'mudzi wa Davide kholo lace; nakhala mfumu m'malo mwace Ahazi mwana wace.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:38 nkhani