2 Mafumu 16:1 BL92

1 Caka cakhumi mphambu zisanu ndi ziwiri ca Peka mwana wa Remaliya Ahazi mwana wa Yotamu mfumu ya Yuda analowa ufumu wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 16

Onani 2 Mafumu 16:1 nkhani