2 Mafumu 16:2 BL92

2 Ahazi anali wa zaka makumi awiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka khumi mphambu zisanu ndi cimodzi m'Yerusalemu; koma sanacita zoongoka pamaso pa Yehova Mulungu wace, ngati Davide kholo lace;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 16

Onani 2 Mafumu 16:2 nkhani