2 Mafumu 16:3 BL92

3 popeza anayenda m'njira ya mafumu a Israyeli, napititsanso mwana wace pamoto, monga mwa zonyansa za amitundu amene Yehova anawaingitsa pamaso pa ana a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 16

Onani 2 Mafumu 16:3 nkhani