7 Nagona Azariya ndi makolo ace, namuika ndi makolo ace m'mudzi wa Davide; nakhala mfumu m'malo mwace Yotamu mwana wace.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:7 nkhani