8 Caka ca makumi atatu mphambu zisanu ndi zitatu ca Azariya mfumu ya Yuda, Zekariya mwana wa Yerobiamu anakhala mfumu ya Israyeli m'Samariya miyezi isanu ndi umodzi.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:8 nkhani