9 Nacita iye coipa pamaso pa Yehova, monga adacita makolo ace; sanaleka zolakwa zace za Yerobiamu mwana wa Nebati, zimene analakwitsa nazo Israyeli.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15
Onani 2 Mafumu 15:9 nkhani