2 Mafumu 16:12 BL92

12 Atafika mfumu kucokera ku Damasiko, anapenya mfumu guwa la nsembelo, nayandikiza mfumu ku guwa la nsembelo, napereka nsembe pomwepo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 16

Onani 2 Mafumu 16:12 nkhani