2 Mafumu 16:13 BL92

13 Nafukiza nsembe yace yopsereza ndi nsemba yace yaufa, natsanulira nsembe yace yothira, nawaza mwazi wa nsembe zace zamtendere pa guwa la nsembelo,

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 16

Onani 2 Mafumu 16:13 nkhani