8 Natenga Ahazi siliva ndi golidi wopezeka m'nyumba ya Yehova, ndi ku cuma ca nyumba ya mfumu, nazitumiza mtulo kwa mfumu ya Asuri.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 16
Onani 2 Mafumu 16:8 nkhani