2 Mafumu 16:9 BL92

9 Nimmvera mfumu ya Asuri, nikwera kumka ku Damasiko mfumu ya Asuri, niulanda, nipita nao anthu ace andende ku Kiri, nimupha Rezini.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 16

Onani 2 Mafumu 16:9 nkhani